2 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli kuti:+ “Tenga mphatso,+ upite kukakumana ndi munthu wa Mulungu woonayo. Ukafunsire+ mawu a Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”
8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli kuti:+ “Tenga mphatso,+ upite kukakumana ndi munthu wa Mulungu woonayo. Ukafunsire+ mawu a Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”