Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Sauli anafunsa mtumiki wakeyo kuti: “Ndiye tikapita kumeneko tikam’patsa chiyani?+ Tilibe mphatso+ imene tingapatse munthu wa Mulungu woonayo, chifukwanso mkate watha m’zotengera zathu. Tili ndi chiyani?”

  • 1 Mafumu 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako mfumuyo inauza munthuyo kuti: “Tiyeni kunyumba mukadye chakudya,+ ndiponso ndikakupatseni mphatso.”+

  • 2 Mafumu 4:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ndiyeno kunabwera munthu wina kuchokera ku Baala-salisa.+ Iye anabweretsera+ munthu wa Mulungu woonayo mkate wa zipatso zoyambirira kucha,+ mitanda 20 ya mkate wa balere,+ ndi tirigu* watsopano m’thumba lake. Choncho Elisa anati: “Gawira anthuwa kuti adye.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena