-
Yeremiya 40:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma Yeremiya anali asanaganize zobwerera pamene Nebuzaradani anamuuza kuti: “Bwerera kwa Gedaliya,+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ amene mfumu ya Babulo yamuika kukhala wolamulira mizinda ya Yuda. Ukakhale naye pakati pa anthu ako ndipo ukapite kulikonse kumene ungakonde kupita.”+
Pamenepo mkulu wa asilikali olondera mfumu anamupatsa chakudya chapaulendo ndi mphatso ndipo anamulola kupita.+
-