Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ezara ameneyu ananyamuka n’kuchoka ku Babulo. Iye anali katswiri wodziwa kukopera+ chilamulo cha Mose,+ chimene Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka. Chotero mfumu inamupatsa zopempha zake zonse chifukwa dzanja la Yehova Mulungu wake linali pa iye.+

  • Miyambo 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+

  • Miyambo 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+

  • Yeremiya 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti: “Ndithu, ndidzakuchitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzakuthandiza kuti ndikupulumutse kwa adani ako pa nthawi ya tsoka+ ndi nthawi ya nsautso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena