Deuteronomo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu. Deuteronomo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+ Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+
5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.
5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+