Deuteronomo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndiwo mawu amene Mose analankhula ndi Aisiraeli onse m’chipululu, m’chigawo cha Yorodano,+ m’chipululu moyang’anana ndi Sufu, pakati pa Parana,+ Tofeli, Labani, Hazeroti+ ndi Dizahabi, Deuteronomo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli,+
1 Awa ndiwo mawu amene Mose analankhula ndi Aisiraeli onse m’chipululu, m’chigawo cha Yorodano,+ m’chipululu moyang’anana ndi Sufu, pakati pa Parana,+ Tofeli, Labani, Hazeroti+ ndi Dizahabi,
10 “Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli,+