Numeri 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nawonso ana a Isiraeli ananyamuka mwa dongosolo lawo lonyamukira.+ Ananyamuka m’chipululu cha Sinai, ndipo mtambowo unakaima m’chipululu cha Parana.+
12 Nawonso ana a Isiraeli ananyamuka mwa dongosolo lawo lonyamukira.+ Ananyamuka m’chipululu cha Sinai, ndipo mtambowo unakaima m’chipululu cha Parana.+