Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 40:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+

  • Numeri 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Yuda alipo 186,400. Amenewa azikhala oyamba kunyamuka.+

  • Numeri 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Rubeni alipo 151,450. Amenewa azikhala achiwiri kunyamuka.+

  • Numeri 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la msasa wa Alevi+ lizikhala pakati pa magulu a misasa ina.

      “Dongosolo limene azilitsatira posamuka,+ n’limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense m’malo ake, malinga ndi chigawo chawo cha mafuko atatu.

  • Numeri 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Efuraimu alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+

  • Numeri 2:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Dani alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ malinga ndi zigawo za Aisiraeli za mafuko atatuatatu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena