Genesis 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anakhalabe m’chipululu cha Parana,+ ndipo amayi ake anakamutengera mkazi kudziko la Iguputo. Numeri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pake, anthuwo anachoka ku Hazeroti,+ n’kukamanga msasa m’chipululu cha Parana.+ Numeri 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo. Deuteronomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mtunda woyenda masiku 11 kuchokera ku Horebe kudzera njira ya kuphiri la Seiri yopita ku Kadesi-barinea.+
26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo.
2 mtunda woyenda masiku 11 kuchokera ku Horebe kudzera njira ya kuphiri la Seiri yopita ku Kadesi-barinea.+