Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Kenako tinachoka ku Horebe ndi kuyenda kudutsa chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha chonse chija+ chimene munachiona, podzera njira ya m’dera lamapiri la Aamori,+ monga momwe Yehova Mulungu wathu anatilamulira, mpaka tinafika ku Kadesi-barinea.+

  • Yoswa 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano ana a Yuda anapita kwa Yoswa ku Giligala.+ Ndipo Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi,+ anauza Yoswa kuti: “Inu mukudziwa bwino za mawu amene Yehova analankhula+ kwa Mose munthu wa Mulungu woona,+ onena za ine ndi inu ku Kadesi-barinea.+

  • Salimo 29:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Liwu la Yehova likuchititsa chipululu kuphiriphitha,+

      Yehova akuchititsa chipululu cha Kadesi+ kuphiriphitha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena