Yesaya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha zimenezi, ndidzachititsa kuti kumwamba kugwedezeke+ ndipo dziko lapansi lidzanjenjemera n’kuchoka m’malo mwake, chifukwa cha ukali wa Yehova wa makamu,+ pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.+ Aheberi 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokhali.”+
13 Chifukwa cha zimenezi, ndidzachititsa kuti kumwamba kugwedezeke+ ndipo dziko lapansi lidzanjenjemera n’kuchoka m’malo mwake, chifukwa cha ukali wa Yehova wa makamu,+ pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.+
26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokhali.”+