Hagai 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+ Hagai 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Uza Zerubabele bwanamkubwa wa Yuda kuti,+ ‘Ine ndigwedeza kumwamba ndi dziko lapansi.+
6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+