Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Yesaya 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti pakangodutsa kanthawi kochepa, kudzudzulako+ kudzatha ndipo mkwiyo wanga udzawayakira, moti adzatha.+ Aheberi 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano, mawu akuti “Ndidzagwedezanso,” akusonyeza kuti zinthu zimene adzazigwedezezo zidzachotsedwa. Zimenezi ndi zinthu zimene zinapangidwa ndi winawake,+ ndipo adzazichotsa kuti zimene sizikugwedezeka zitsale.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+
25 Pakuti pakangodutsa kanthawi kochepa, kudzudzulako+ kudzatha ndipo mkwiyo wanga udzawayakira, moti adzatha.+
27 Tsopano, mawu akuti “Ndidzagwedezanso,” akusonyeza kuti zinthu zimene adzazigwedezezo zidzachotsedwa. Zimenezi ndi zinthu zimene zinapangidwa ndi winawake,+ ndipo adzazichotsa kuti zimene sizikugwedezeka zitsale.+