Hagai 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+ Aheberi 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokhali.”+
6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+
26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokhali.”+