Numeri 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma sindikutero ndi mtumiki wanga Mose.+ Iye ndamuikiza nyumba yanga yonse.+ Deuteronomo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano ili ndi dalitso+ limene Mose, munthu wa Mulungu woona,+ anadalitsa nalo ana a Isiraeli iye asanafe. Salimo 90:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Pemphero la Mose, munthu wa Mulungu woona.+
33 Tsopano ili ndi dalitso+ limene Mose, munthu wa Mulungu woona,+ anadalitsa nalo ana a Isiraeli iye asanafe.