Genesis 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+ Luka 24:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo anawatsogolera kupita nawo ku Betaniya. Kumeneko anakweza manja ake ndi kuwadalitsa.+
28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+