Deuteronomo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano ili ndi dalitso+ limene Mose, munthu wa Mulungu woona,+ anadalitsa nalo ana a Isiraeli iye asanafe.
33 Tsopano ili ndi dalitso+ limene Mose, munthu wa Mulungu woona,+ anadalitsa nalo ana a Isiraeli iye asanafe.