Yoswa 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo monga momwe anawalonjezera.+ Chotero bwererani, mupite kumahema anu m’dziko lanu, limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani kutsidya lina la Yorodano.+
4 Tsopano Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo monga momwe anawalonjezera.+ Chotero bwererani, mupite kumahema anu m’dziko lanu, limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani kutsidya lina la Yorodano.+