-
Nehemiya 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ezara wokopera Malembayo, anaimirira pansanja yamatabwa+ imene inamangidwa chifukwa cha mwambo umenewu. Pafupi naye, kudzanja lake lamanja kunaimirira Matitiya, Sema, Anaya, Uriya, Hilikiya, ndi Maaseya. Ndipo kudzanja lake lamanzere kunaimirira Pedaya, Misayeli, Malikiya,+ Hasumu,+ Hasi-badana, Zekariya ndi Mesulamu.
-