Ekisodo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo ndidzalola Farao kuumitsa mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzapezerapo ulemerero mwa kugonjetsa Farao ndi magulu ake onse ankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi momwemo. Ezara 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atamandike Yehova Mulungu wa makolo athu,+ amene waika maganizo amenewa mumtima+ mwa mfumu, kuti nyumba ya Yehova imene ili ku Yerusalemu ikongoletsedwe.+ Salimo 106:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapoloAwamvere chisoni.+
4 Pamenepo ndidzalola Farao kuumitsa mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzapezerapo ulemerero mwa kugonjetsa Farao ndi magulu ake onse ankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi momwemo.
27 Atamandike Yehova Mulungu wa makolo athu,+ amene waika maganizo amenewa mumtima+ mwa mfumu, kuti nyumba ya Yehova imene ili ku Yerusalemu ikongoletsedwe.+