Salimo 96:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+ Yesaya 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+ Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Yesaya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa, 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+
10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+
6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+
5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+