Yesaya 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+ Yesaya 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba.+ Ndinenso womaliza.+ Chivumbulutso 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Alefa ndi Omega,+ woyamba ndi wotsiriza, chiyambi ndi mapeto.+
4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+
12 “Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba.+ Ndinenso womaliza.+