Salimo 90:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ntchito zanu zionekere kwa atumiki anu,+Ndipo ulemerero wanu uonekere pa ana awo.+ Salimo 111:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zochita zake+ n’zaulemerero ndi ulemu,+ו [Waw]Ndipo chilungamo chake chidzakhalapobe kwamuyaya.+ Yohane 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawauza kuti: “Atate wanga akugwirabe ntchito mpaka pano, inenso ndikugwirabe ntchito.”+
17 Koma iye anawauza kuti: “Atate wanga akugwirabe ntchito mpaka pano, inenso ndikugwirabe ntchito.”+