Ekisodo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+ 1 Mbiri 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake,+Pokhala pake pali mphamvu ndi chimwemwe.+ Yobu 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tadziveka ukulu+ ndiponso kukwezeka,+Ndipo uvale ulemu+ ndi ulemerero.+ Salimo 145:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti ana a anthu adziwe za ntchito zanu zamphamvu+Ndi kukula kwa ulemerero wa ufumu wanu.+
6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+