Yesaya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lowani muthanthwe ndipo dzibiseni m’fumbi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+ Yesaya 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzafuula mosangalala. Adzafuula mokondwa ali kunyanja, chifukwa cha kukwezeka kwa Yehova.+
10 Lowani muthanthwe ndipo dzibiseni m’fumbi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+