1 Mbiri 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake,+Pokhala pake pali mphamvu ndi chimwemwe.+ Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+