Salimo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+ Salimo 60:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti okondedwa anu apulumutsidwe,+Tipulumutseni ndi dzanja lanu lamanja ndi kutiyankha.+ Salimo 89:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkono wamphamvu ndi wanu,+Dzanja lanu ndi lamphamvu,+Dzanja lanu lamanja ndi lokwezeka.+ Salimo 118:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+ 1 Petulo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho dzichepetseni pansi pa dzanja lamphamvu la Mulungu, kuti adzakukwezeni m’nthawi yake.+
7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+
15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+