Salimo 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adalitsike,+Pakuti wandisonyeza modabwitsa kukoma mtima kosatha+ mumzinda wozingidwa ndi adani.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
21 Yehova adalitsike,+Pakuti wandisonyeza modabwitsa kukoma mtima kosatha+ mumzinda wozingidwa ndi adani.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+