Salimo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+ Luka 24:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Pamenepo anamugwadira ndi kubwerera ku Yerusalemu ali ndi chimwemwe chochuluka.+
11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+ Luka 24:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Pamenepo anamugwadira ndi kubwerera ku Yerusalemu ali ndi chimwemwe chochuluka.+