Salimo 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inu mudzandipatsa chishango chanu cha chipulumutso,+Dzanja lanu lamanja lidzandichirikiza,+Ndipo kudzichepetsa kwanu n’kumene kudzandikweza.+ Salimo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.+Dzanja lanu lamanja lidzapeza odana nanu. Salimo 118:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+ Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+
35 Inu mudzandipatsa chishango chanu cha chipulumutso,+Dzanja lanu lamanja lidzandichirikiza,+Ndipo kudzichepetsa kwanu n’kumene kudzandikweza.+
15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+
10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+