2 Samueli 22:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Inu mudzandipatsa chishango chanu cha chipulumutso,+Ndipo kudzichepetsa kwanu n’kumene kumandikweza.+ Salimo 113:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye amatsika m’munsi kuti aone kumwamba ndi dziko lapansi.+
36 Inu mudzandipatsa chishango chanu cha chipulumutso,+Ndipo kudzichepetsa kwanu n’kumene kumandikweza.+