Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+

      Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+

  • Salimo 18:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Inu mudzandipatsa chishango chanu cha chipulumutso,+

      Dzanja lanu lamanja lidzandichirikiza,+

      Ndipo kudzichepetsa kwanu n’kumene kudzandikweza.+

  • Salimo 102:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye wayang’ana pansi ali kumalo oyera, okwezeka,+

      Yehova wayang’ana dziko lapansi ali kumwambako,+

  • Salimo 138:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+

      Koma wodzikuza samuyandikira.+

  • Yesaya 66:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena