Genesis 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, Yehova anatsikirako kukaona mzinda ndi nsanja imene ana a anthu anali kumanga.+ Salimo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana,+Waona ana onse a anthu.+ Salimo 102:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye wayang’ana pansi ali kumalo oyera, okwezeka,+Yehova wayang’ana dziko lapansi ali kumwambako,+