Salimo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana,+Waona ana onse a anthu.+ Salimo 113:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye amatsika m’munsi kuti aone kumwamba ndi dziko lapansi.+