Salimo 37:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+ Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Isiraeli, khulupirira Yehova.+Iye ndiye thandizo lako ndi chishango chako.+ Salimo 121:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Thandizo langa lichokera kwa Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+
40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+