Salimo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+
13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+
17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+