Salimo 70:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+
5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+