Salimo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+ Salimo 69:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ine ndasautsika ndipo ndikumva kupweteka.+Inu Mulungu, chipulumutso chanu chinditeteze.+ Salimo 109:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndasautsika ndipo ndasauka,+Mtima wanga walasika mkati mwanga.+
17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+