Salimo 70:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndine munthu wovutika komanso wosauka.+Inu Mulungu, ndithandizeni mwamsanga.+ Inu ndi amene mumandithandiza komanso kundipulumutsa.+Inu Yehova musachedwe.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 70:5 Nsanja ya Olonda,5/15/1991, tsa. 23
5 Koma ine ndine munthu wovutika komanso wosauka.+Inu Mulungu, ndithandizeni mwamsanga.+ Inu ndi amene mumandithandiza komanso kundipulumutsa.+Inu Yehova musachedwe.+