Salimo 70:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 70:5 Nsanja ya Olonda,5/15/1991, tsa. 23
5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+