Yesaya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.” Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+ 1 Akorinto 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira.
5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.”
4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+
13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira.