Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 64:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu onse adzachita mantha,+Ndipo adzanena za ntchito za Mulungu,+Iwo adzamvetsa bwino ntchito zake.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
9 Anthu onse adzachita mantha,+Ndipo adzanena za ntchito za Mulungu,+Iwo adzamvetsa bwino ntchito zake.+