1 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene sanafe anakanthidwa ndi matenda a mudzi.+ Ndipo anthu a mumzindawo anayang’ana kumwamba, kulirira+ thandizo. Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+ Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
12 Anthu amene sanafe anakanthidwa ndi matenda a mudzi.+ Ndipo anthu a mumzindawo anayang’ana kumwamba, kulirira+ thandizo.
43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+