Salimo 145:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu adzanena za zochita zanu zamphamvu ndi zochititsa mantha.+Ndipo ine ndidzalengeza za ukulu wanu.+ Yeremiya 50:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa komanso amene apulumuka m’dziko la Babulo+ kuti akanene ku Ziyoni za chilango chimene Yehova Mulungu wathu akubwezera.+ Iye akubwezera kuwonongedwa kwa kachisi wake.+ Yeremiya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova watichitira zinthu zachilungamo.+ Bwerani kuti tisimbe ntchito za Yehova Mulungu wathu mu Ziyoni.”+
6 Anthu adzanena za zochita zanu zamphamvu ndi zochititsa mantha.+Ndipo ine ndidzalengeza za ukulu wanu.+
28 “Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa komanso amene apulumuka m’dziko la Babulo+ kuti akanene ku Ziyoni za chilango chimene Yehova Mulungu wathu akubwezera.+ Iye akubwezera kuwonongedwa kwa kachisi wake.+
10 Yehova watichitira zinthu zachilungamo.+ Bwerani kuti tisimbe ntchito za Yehova Mulungu wathu mu Ziyoni.”+