Yoswa 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+ Nehemiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.
9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+
5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.