Yeremiya 51:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 chifukwa Yehova akufunkha zinthu za Babulo ndi kuthetsa mawu ake aakulu.+ Mafunde awo adzachita phokoso ngati madzi ambiri.+ Komanso phokoso la mawu awo lidzamveka m’Babulo.
55 chifukwa Yehova akufunkha zinthu za Babulo ndi kuthetsa mawu ake aakulu.+ Mafunde awo adzachita phokoso ngati madzi ambiri.+ Komanso phokoso la mawu awo lidzamveka m’Babulo.