Salimo 107:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+ Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+
21 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+