Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 “Koma mukupitirizabe kukhala ndi moyo chifukwa anakonda makolo anu ndipo anasankha mbewu zawo zobwera pambuyo pawo,+ ndi kukutulutsani mu Iguputo ndi mphamvu zake zazikulu,+ komanso anali kukuyang’anirani.

  • Deuteronomo 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Yehova anadziphatika kwa makolo anu ndi kuwakonda, moti anasankha ana awo obadwa m’mbuyo mwawo,+ inuyo, pakati pa anthu onse monga mmene zilili lero.

  • Salimo 78:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+

      Phiri la Ziyoni limene analikonda.+

  • Mateyu 24:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Ndani kwenikweni amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru+ amene mbuye wake anamuika kuti aziyang’anira antchito ake apakhomo, ndi kuwapatsa chakudya pa nthawi yoyenera?+

  • Aefeso 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+

  • 2 Atesalonika 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Komabe, tiyeneradi kumayamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu abale okondedwa ndi Yehova. Tiyenera kutero chifukwa Mulungu anakusankhani+ kuchokera pachiyambi kuti mudzapulumuke mwa kukuyeretsani+ ndi mzimu,+ ndiponso mwa chikhulupiriro chanu m’choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena