Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Akolose 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chimene muli nacho chifukwa cha chiyembekezo+ chodzalandira zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi pamene choonadi cha uthenga wabwino chinalengezedwa kwa inu.+ 1 Timoteyo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amenewo adzaletsa anthu kukwatira,+ ndipo adzalamula anthu kusala zakudya zina+ zimene Mulungu anazilenga+ kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro ndiponso odziwa choonadi molondola azidya moyamikira.+ 2 Yohane 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Timakukondani chifukwa cha choonadi chimene chili mumtima mwathu,+ ndipo chidzakhalabe ndi ife mpaka muyaya.+
5 chimene muli nacho chifukwa cha chiyembekezo+ chodzalandira zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi pamene choonadi cha uthenga wabwino chinalengezedwa kwa inu.+
3 Anthu amenewo adzaletsa anthu kukwatira,+ ndipo adzalamula anthu kusala zakudya zina+ zimene Mulungu anazilenga+ kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro ndiponso odziwa choonadi molondola azidya moyamikira.+
2 Timakukondani chifukwa cha choonadi chimene chili mumtima mwathu,+ ndipo chidzakhalabe ndi ife mpaka muyaya.+