1 Timoteyo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthuwa amaletsa kukwatira,+ ndipo amalamula anthu kuti azisala zakudya+ zimene Mulungu anazilenga kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro+ ndiponso odziwa choonadi molondola azidya+ nʼkuyamikira Mulungu. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,7/1/1996, ptsa. 6-712/15/1990, tsa. 21
3 Anthuwa amaletsa kukwatira,+ ndipo amalamula anthu kuti azisala zakudya+ zimene Mulungu anazilenga kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro+ ndiponso odziwa choonadi molondola azidya+ nʼkuyamikira Mulungu.